Yesaya 29:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsoka kwa anthu amene abisa patali kwambiri zolinga zawo, pozibisira Yehova,+ amene zochita zawo zimachitikira m’malo a mdima,+ ndipo amati: “Ndani akutiona, ndipo ndani akudziwa zimene tikuchita?”+ Hoseya 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo adzadya koma sadzakhuta.+ Adzachita zachiwerewere ndi akazi koma sadzachulukana+ chifukwa chakuti asiya kumvera Yehova.+ 1 Atesalonika 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho munthu wonyalanyaza+ chiphunzitso chimenechi sakunyalanyaza munthu, koma Mulungu+ amene amaika mzimu wake woyera+ mwa inu.
15 Tsoka kwa anthu amene abisa patali kwambiri zolinga zawo, pozibisira Yehova,+ amene zochita zawo zimachitikira m’malo a mdima,+ ndipo amati: “Ndani akutiona, ndipo ndani akudziwa zimene tikuchita?”+
10 Iwo adzadya koma sadzakhuta.+ Adzachita zachiwerewere ndi akazi koma sadzachulukana+ chifukwa chakuti asiya kumvera Yehova.+
8 Choncho munthu wonyalanyaza+ chiphunzitso chimenechi sakunyalanyaza munthu, koma Mulungu+ amene amaika mzimu wake woyera+ mwa inu.