Yesaya 41:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndidzatsegula mitsinje pamapiri opanda zomera zilizonse, ndipo pakatikati pa zigwa ndidzatsegulapo akasupe.+ Chipululu ndidzachisandutsa dambo lamadzi, ndipo dziko lopanda madzi ndidzalisandutsa pochokera madzi.+ Yesaya 44:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti ndidzapatsa madzi munthu waludzu,+ ndipo ndidzaika timitsinje tamadzi pamalo ouma.+ Ndidzatsanulira mzimu wanga pambewu yako+ ndi madalitso anga pa mbadwa zako.
18 Ndidzatsegula mitsinje pamapiri opanda zomera zilizonse, ndipo pakatikati pa zigwa ndidzatsegulapo akasupe.+ Chipululu ndidzachisandutsa dambo lamadzi, ndipo dziko lopanda madzi ndidzalisandutsa pochokera madzi.+
3 Pakuti ndidzapatsa madzi munthu waludzu,+ ndipo ndidzaika timitsinje tamadzi pamalo ouma.+ Ndidzatsanulira mzimu wanga pambewu yako+ ndi madalitso anga pa mbadwa zako.