Salimo 46:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pali mtsinje womwe nthambi zake zimachititsa anthu a mumzinda wa Mulungu kukondwera,+Chihema chachikulu chopatulika koposa cha Wam’mwambamwamba.+ Yesaya 30:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 M’tsiku limene anthu ambiri adzaphedwe ndiponso limene nsanja zidzagwe, paphiri lililonse lalitali ndi paphiri lililonse laling’ono padzakhala timitsinje+ ndi ngalande zamadzi.+ Yoweli 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Nthawi imeneyo mapiri adzachucha vinyo wotsekemera.+ Mkaka udzayenda pazitunda ndipo m’mitsinje yonse ya Yuda mudzayenda madzi. Kasupe wamadzi adzatuluka m’nyumba ya Yehova+ ndi kuthirira chigwa cha Mitengo ya Mthethe.+
4 Pali mtsinje womwe nthambi zake zimachititsa anthu a mumzinda wa Mulungu kukondwera,+Chihema chachikulu chopatulika koposa cha Wam’mwambamwamba.+
25 M’tsiku limene anthu ambiri adzaphedwe ndiponso limene nsanja zidzagwe, paphiri lililonse lalitali ndi paphiri lililonse laling’ono padzakhala timitsinje+ ndi ngalande zamadzi.+
18 “Nthawi imeneyo mapiri adzachucha vinyo wotsekemera.+ Mkaka udzayenda pazitunda ndipo m’mitsinje yonse ya Yuda mudzayenda madzi. Kasupe wamadzi adzatuluka m’nyumba ya Yehova+ ndi kuthirira chigwa cha Mitengo ya Mthethe.+