2 Mafumu 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iwe wanena kuti (koma ndi mawu a pakamwa chabe), ‘Ine ndili ndi nzeru+ ndi mphamvu zofunika pankhondo.’ Kodi ukudalira ndani popandukira+ ine? Salimo 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zochita zake zimayenda bwino nthawi zonse.+Zigamulo zanu zili pamwamba kwambiri pamene iye sangathe kuziona.+Onse omuchitira zoipa amawanyodola.+
20 Iwe wanena kuti (koma ndi mawu a pakamwa chabe), ‘Ine ndili ndi nzeru+ ndi mphamvu zofunika pankhondo.’ Kodi ukudalira ndani popandukira+ ine?
5 Zochita zake zimayenda bwino nthawi zonse.+Zigamulo zanu zili pamwamba kwambiri pamene iye sangathe kuziona.+Onse omuchitira zoipa amawanyodola.+