Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 18:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Yehova anakhala naye,+ ndipo kulikonse kumene ankapita anali kuchita zinthu mwanzeru.+ Anapandukira mfumu ya Asuri n’kukana kuitumikira.+

  • Ezara 4:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 n’cholinga choti mufufuze m’buku la mbiri+ ya makolo anu. Mukafufuza m’bukulo mupeza kuti mzinda umenewu ndi mzinda woukira ndi wowonongetsa chuma cha mafumu ndi zigawo za mayiko. Mupezanso kuti mumzinda umenewu mwakhala muli anthu oyambitsa kupanduka kuyambira kalekale. N’chifukwa chake mzindawu uli bwinja.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena