Esitere 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho nkhani imeneyi anaifufuza ndipo pamapeto pake zonse zinadziwika, ndipo onse awiri, Bigitana ndi Teresi anapachikidwa+ pamtengo.+ Kenako zimenezi zinalembedwa pamaso pa mfumu m’buku la zochitika+ za m’masiku amenewo. Esitere 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Usiku umenewo mfumu inasowa tulo.+ Choncho inaitanitsa buku limene anali kulembamo zochitika+ za m’masiku amenewo. Ndiyeno anawerenga zochitikazo pamaso pa mfumu.
23 Choncho nkhani imeneyi anaifufuza ndipo pamapeto pake zonse zinadziwika, ndipo onse awiri, Bigitana ndi Teresi anapachikidwa+ pamtengo.+ Kenako zimenezi zinalembedwa pamaso pa mfumu m’buku la zochitika+ za m’masiku amenewo.
6 Usiku umenewo mfumu inasowa tulo.+ Choncho inaitanitsa buku limene anali kulembamo zochitika+ za m’masiku amenewo. Ndiyeno anawerenga zochitikazo pamaso pa mfumu.