2 Mafumu 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 M’chaka cha 14 cha Mfumu Hezekiya, Senakeribu+ mfumu ya Asuri+ anabwera kudzachita nkhondo ndi mizinda yonse ya Ayuda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri, ndipo analanda mizindayo. Yesaya 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Iye waukira Ayati.+ Wadutsa ku Migironi. Waika katundu wake ku Mikimasi.+ Yesaya 33:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Misewu ikuluikulu yawonongeka.+ Palibenso munthu woyenda m’njira.+ Iye waphwanya pangano+ ndipo wanyansidwa ndi mizinda.+ Sasamala za munthu aliyense.+
13 M’chaka cha 14 cha Mfumu Hezekiya, Senakeribu+ mfumu ya Asuri+ anabwera kudzachita nkhondo ndi mizinda yonse ya Ayuda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri, ndipo analanda mizindayo.
8 Misewu ikuluikulu yawonongeka.+ Palibenso munthu woyenda m’njira.+ Iye waphwanya pangano+ ndipo wanyansidwa ndi mizinda.+ Sasamala za munthu aliyense.+