Yesaya 10:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Iye wadula ndi nkhwangwa zitsamba zowirira za m’nkhalango, ndipo wamphamvu adzagwetsa mitengo ya ku Lebanoni.+ Ezekieli 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Wafanana ndi Msuri. Wafanana ndi mtengo wa mkungudza wa ku Lebanoni,+ wanthambi zikuluzikulu zokongola,+ wanthambi za masamba ambiri zopereka mthunzi, mtengo wautali kwambiri+ umene nsonga yake inafika m’mitambo.+
34 Iye wadula ndi nkhwangwa zitsamba zowirira za m’nkhalango, ndipo wamphamvu adzagwetsa mitengo ya ku Lebanoni.+
3 Wafanana ndi Msuri. Wafanana ndi mtengo wa mkungudza wa ku Lebanoni,+ wanthambi zikuluzikulu zokongola,+ wanthambi za masamba ambiri zopereka mthunzi, mtengo wautali kwambiri+ umene nsonga yake inafika m’mitambo.+