Yesaya 27:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 M’masiku amene akubwerawo, Yakobo adzamera mizu n’kukhala wamphamvu ngati mtengo. Isiraeli+ adzakhala ngati mtengo waukulu wa maluwa ambiri. Iwo adzabereka zipatso panthaka ya dziko lonse lapansi.+ Yesaya 60:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anthu ako onse adzakhala olungama.+ Iwo adzakhala m’dzikomo mpaka kalekale.+ Anthuwo adzakhala mmera wobzalidwa ndi ine+ ndiponso ntchito ya manja anga,+ kuti ineyo ndikongoletsedwe.+ Yoweli 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno Yehova adzachitira nsanje dziko lake+ ndipo adzamvera chifundo anthu ake.+
6 M’masiku amene akubwerawo, Yakobo adzamera mizu n’kukhala wamphamvu ngati mtengo. Isiraeli+ adzakhala ngati mtengo waukulu wa maluwa ambiri. Iwo adzabereka zipatso panthaka ya dziko lonse lapansi.+
21 Anthu ako onse adzakhala olungama.+ Iwo adzakhala m’dzikomo mpaka kalekale.+ Anthuwo adzakhala mmera wobzalidwa ndi ine+ ndiponso ntchito ya manja anga,+ kuti ineyo ndikongoletsedwe.+