Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 44:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Munthu wogoba zitsulo ndi chogobera watentha chitsulocho ndi makala amoto. Wachiwongola ndi nyundo, ndipo wakhala ali jijirijijiri kuchiumba ndi dzanja lake lamphamvu.+ Wamva njala ndipo alibe mphamvu. Sanamwe madzi, chotero watopa.

  • Yesaya 46:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pali anthu amene amakhuthula golide m’zikwama, ndi kuyeza siliva pasikelo. Iwo amalemba ganyu mmisiri wa zitsulo ndipo iye amapanga mulungu ndi zinthu zimenezi.+ Kenako anthuwo amayamba kuweramira ndi kugwadira mulunguyo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena