Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 40:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mmisiri wapanga chifaniziro chopangidwa ndi chitsulo chosungunula.+ Mmisiri wina wa zitsulo wachikuta ndi golide,+ ndipo akuchipangira matcheni asiliva.+

  • Yesaya 41:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Chotero mmisiri wa mitengo anali kulimbikitsa mmisiri wa zitsulo.+ Amene anali kusalaza zitsulo ndi nyundo anali kulimbikitsa amene anali kumenya zitsulo ndi nyundo. Ponena za ntchito yowotcherera zitsulo ndi mtovu, iye anati: “Zili bwino.” Pomalizira pake, wina anakhomerera fanolo ndi misomali kuti lisagwedezeke.+

  • Yesaya 46:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pali anthu amene amakhuthula golide m’zikwama, ndi kuyeza siliva pasikelo. Iwo amalemba ganyu mmisiri wa zitsulo ndipo iye amapanga mulungu ndi zinthu zimenezi.+ Kenako anthuwo amayamba kuweramira ndi kugwadira mulunguyo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena