Deuteronomo 32:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Akanakhala anzeru,+ akanaganizira mozama zimenezi.+Akanalingalira kuti ziwathera bwanji.+ Miyambo 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mwana wanga, ukamvera mawu anga+ ndi kusunga malamulo anga ngati chuma chamtengo wapatali,+ Yesaya 44:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iwo sadziwa chilichonse+ ndipo samvetsetsa chilichonse+ chifukwa maso awo amatidwa kuti asamaone,+ ndipo mitima yawo ndi yosazindikira zinthu.+ Hagai 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Ganizirani mofatsa zimene mukuchita.+
18 Iwo sadziwa chilichonse+ ndipo samvetsetsa chilichonse+ chifukwa maso awo amatidwa kuti asamaone,+ ndipo mitima yawo ndi yosazindikira zinthu.+