Yeremiya 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Onse pamodzi ndi opanda nzeru ndiponso opusa.+ Mtengo umangowalimbikitsa kuchita zachabechabe.+ Aroma 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chifukwa chakuti, ngakhale anam’dziwa Mulungu, iwo sanam’patse ulemerero monga Mulungu kapena kumuyamikira.+ M’malomwake anayamba kulingalira zinthu zopanda pake+ ndipo mtima wawo wopusawo unachita mdima.+
21 Chifukwa chakuti, ngakhale anam’dziwa Mulungu, iwo sanam’patse ulemerero monga Mulungu kapena kumuyamikira.+ M’malomwake anayamba kulingalira zinthu zopanda pake+ ndipo mtima wawo wopusawo unachita mdima.+