Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 115:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Amene amawapanga adzafanana nawo.+

      Onse amene amawakhulupirira adzakhala ngati mafanowo.+

  • Yesaya 41:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Onsewo ali ngati chinthu choti kulibeko. Ntchito zawo si kanthu. Mafano awo opangidwa ndi zitsulo zosungunula ali ngati mphepo ndiponso zinthu zomwe si zenizeni.+

  • Yeremiya 51:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Munthu aliyense wachita zinthu mopanda nzeru kwambiri moti ndi zoonekeratu kuti sakudziwa kalikonse.+ Mmisiri aliyense wa zitsulo adzachita manyazi chifukwa cha chifaniziro chake chosula.+ Pakuti chifaniziro chake chopangidwa ndi chitsulo chosungunula ndi mulungu wonama+ ndipo mafano amenewa alibe moyo.+

  • Habakuku 2:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Kodi chifaniziro chosema, chifaniziro chopangidwa ndi chitsulo chosungunula ndiponso mphunzitsi wonama,+ zili ndi phindu lanji+ kuti wozipanga azizikhulupirira+ ndipo azipanga milungu yopanda pake yosalankhula?+

  • Zekariya 10:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Aterafi*+ amalankhula zoipa. Ochita zamaula amaona masomphenya onama+ ndipo amafotokoza maloto opanda pake. Iwo saphula kanthu polimbikitsa anthu.+ N’chifukwa chake adzasochere ngati nkhosa.+ Iwo adzavutika chifukwa adzakhala opanda m’busa.+

  • Aroma 1:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ngakhale anali kunena motsimikiza kuti ndi anzeru, iwo anakhala opusa+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena