-
1 Mafumu 3:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Popeza mtima wa mayi yemwe mwana wake anali wamoyoyo unayamba kugunda kwambiri+ chifukwa cha mwana wakeyo,+ nthawi yomweyo anauza mfumuyo kuti: “Pepani+ mbuyanga! Amuna inu, m’patseni mayiyu mwana wamoyoyu. Musamuphe ayi.” Apa n’kuti mayi wina uja akunena kuti: “Mwanayu sakhala wanga kapena wako. Amuna inu, m’duleni!”+
-