Salimo 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zopweteka zimachuluka kwa anthu amene amati akaona mulungu wina, amamuthamangira.+Ine sindidzatsanula nsembe zawo zachakumwa zothira magazi,+Ndipo sindidzatchula dzina lawo ndi milomo yanga.+ Salimo 32:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Zopweteka za woipa ndi zambiri.Koma wokhulupirira Yehova+ amazunguliridwa ndi kukoma mtima kosatha.+
4 Zopweteka zimachuluka kwa anthu amene amati akaona mulungu wina, amamuthamangira.+Ine sindidzatsanula nsembe zawo zachakumwa zothira magazi,+Ndipo sindidzatchula dzina lawo ndi milomo yanga.+
10 Zopweteka za woipa ndi zambiri.Koma wokhulupirira Yehova+ amazunguliridwa ndi kukoma mtima kosatha.+