Ekisodo 23:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Muzisamalira zonse zimene ndakuuzani,+ ndipo musatchule dzina la milungu ina. Lisamveke pakamwa panu.+ Yoswa 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiponso musayanjane ndi mitundu+ imene yatsala pakati panu. Musamatchule mayina a milungu yawo+ kapena kulumbirira pa milunguyo,+ ndipo musamaitumikire kapena kuigwadira.+ Hoseya 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘Sindidzamulola kutchulanso mayina a zifaniziro za Baala,+ ndipo iye sadzakumbukiranso mayina awo.+
13 “Muzisamalira zonse zimene ndakuuzani,+ ndipo musatchule dzina la milungu ina. Lisamveke pakamwa panu.+
7 Ndiponso musayanjane ndi mitundu+ imene yatsala pakati panu. Musamatchule mayina a milungu yawo+ kapena kulumbirira pa milunguyo,+ ndipo musamaitumikire kapena kuigwadira.+
17 “‘Sindidzamulola kutchulanso mayina a zifaniziro za Baala,+ ndipo iye sadzakumbukiranso mayina awo.+