Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 2:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “‘Ine ndinaphwanya goli lako kukhala zidutswazidutswa kalekale.+ Ndinadula zingwe zimene anakumanga nazo. Koma iwe unati: “Sindikutumikirani,” ndipo unagona motangadza+ paphiri lililonse lalitali ndi pansi pa mtengo uliwonse waukulu wa masamba ambiri obiriwira+ n’kumachita uhule+ pamenepo.

  • Ezekieli 16:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Unatenga zovala zako zina n’kupangira malo okwezeka+ okhala ndi mitundu yosiyanasiyana ndipo unayamba kuchitirapo uhule.+ Zoterezi siziyenera kuchitika. Zisamachitike ayi.

  • Ezekieli 23:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ana aamuna a ku Babulowo anali kubwera kwa iye. Anali kupita kubedi lake lochitirapo zachikondi ndi kumuipitsa ndi chiwerewere chawo.+ Iye anapitiriza kuipitsidwa ndi amunawo kenako ananyansidwa nawo n’kuwasiya.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena