Yesaya 30:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mzimu wa Mulungu uli ngati mtsinje wosefukira umene wafika m’khosi,+ umene iye adzaugwiritsire ntchito posefa+ mitundu ya anthu monga zinthu zopanda pake. Pakamwa pa mitunduyo adzamangapo zingwe ngati zowongolera hatchi,+ zimene zidzawachititse kuyenda uku ndi uku.+ Zekariya 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho iye anandiuza kuti: “Yehova wauza Zerubabele kuti, ‘“Kuti zinthu zonsezi zichitike, sipakufunika gulu lankhondo,+ kapena mphamvu,+ koma mzimu wanga,”+ watero Yehova wa makamu.
28 Mzimu wa Mulungu uli ngati mtsinje wosefukira umene wafika m’khosi,+ umene iye adzaugwiritsire ntchito posefa+ mitundu ya anthu monga zinthu zopanda pake. Pakamwa pa mitunduyo adzamangapo zingwe ngati zowongolera hatchi,+ zimene zidzawachititse kuyenda uku ndi uku.+
6 Choncho iye anandiuza kuti: “Yehova wauza Zerubabele kuti, ‘“Kuti zinthu zonsezi zichitike, sipakufunika gulu lankhondo,+ kapena mphamvu,+ koma mzimu wanga,”+ watero Yehova wa makamu.