Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Mulungu adzakhala woweruza pakati pa mitundu+ ndipo adzakonza zinthu+ zokhudza mitundu yambiri ya anthu.+ Iwo adzasula malupanga awo kuti akhale makasu a pulawo, ndi mikondo yawo kuti ikhale zida zosadzira mitengo.+ Mtundu wa anthu sudzanyamula lupanga kuti umenyane ndi mtundu unzake, ndipo anthuwo sadzaphunziranso nkhondo.+

  • Yesaya 11:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Sizidzavulazana+ kapena kuwonongana m’phiri langa lonse loyera,+ chifukwa dziko lapansi lidzadzaza ndi anthu odziwa Yehova ngati mmene madzi amadzazira nyanja.+

  • Yesaya 54:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Iwe udzakhazikika m’chilungamo.+ Kuponderezedwa udzatalikirana nako,+ ndipo sudzaopa aliyense. Chilichonse choopsa udzatalikirana nacho, pakuti sichidzakuyandikira.+

  • Zekariya 9:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndidzamanga msasa kunja kwa nyumba yanga kuti ndizidzailondera,+ moti sipadzakhalanso munthu wolowa kapena kutuluka. Kapitawo sadzadutsanso pakati pawo+ pakuti ine ndaona ndi maso anga zimene zinawachitikira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena