Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 72:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 M’masiku ake, wolungama adzaphuka,+

      Ndipo padzakhala mtendere wochuluka kwa nthawi yonse pamene mwezi udzakhalepo.+

  • Yesaya 60:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “M’dziko lako simudzamvekanso zachiwawa. Mkati mwa malire ako simudzakhalanso kusakaza kapena kuwononga.+ Mipanda yako udzaitcha Chipulumutso+ ndipo zipata zako udzazitcha Chitamando.

  • Mika 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mulungu adzakhala woweruza pakati pa mitundu yambiri ya anthu+ ndipo adzakonza zinthu+ zokhudza anthu ochokera m’mitundu yamphamvu yakutali.+ Iwo adzasula malupanga awo kuti akhale makasu a pulawo, ndi mikondo yawo kuti ikhale zida zosadzira mitengo.+ Mtundu wa anthu sudzanyamula lupanga kuti umenyane ndi mtundu unzake, ndipo anthuwo sadzaphunziranso nkhondo.+

  • Mateyu 5:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Koma ine ndikukuuzani kuti: Pitirizani kukonda adani anu+ ndi kupempherera amene akukuzunzani,+

  • Mateyu 26:52
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 52 Pamenepo Yesu anamuuza kuti: “Bwezera lupanga lako m’chimake,+ pakuti onse ogwira lupanga adzafa ndi lupanga.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena