2 Mafumu 19:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chifukwa anthu otsala adzachokera ku Yerusalemu,+ ndipo opulumuka adzachokera kuphiri la Ziyoni.+ Yehova wa makamu adzachita zimenezi modzipereka kwambiri.+ Zekariya 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Yehova wa makamu+ wanena kuti: ‘Ziyoni ndidzam’chitira nsanje kwambiri.+ Ndidzam’chitira nsanje ndi kukwiya kwambiri.’”+
31 Chifukwa anthu otsala adzachokera ku Yerusalemu,+ ndipo opulumuka adzachokera kuphiri la Ziyoni.+ Yehova wa makamu adzachita zimenezi modzipereka kwambiri.+
2 “Yehova wa makamu+ wanena kuti: ‘Ziyoni ndidzam’chitira nsanje kwambiri.+ Ndidzam’chitira nsanje ndi kukwiya kwambiri.’”+