Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 9:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ulamuliro wake wangati wa kalonga udzafika kutali+ ndipo mtendere sudzatha+ pampando wachifumu wa Davide+ ndiponso mu ufumu wake, kuti iye achititse ufumuwo kukhazikika+ ndi kukhala wolimba pogwiritsa ntchito chilungamo,+ ndiponso pogwiritsa ntchito mtima wowongoka,+ kuyambira panopa mpaka kalekale.* Yehova wa makamu adzachita zimenezi modzipereka kwambiri.+

  • Yesaya 59:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Choncho iye anavala chilungamo monga chovala chodzitetezera chamamba achitsulo,+ ndiponso anavala chisoti cholimba chachipulumutso kumutu kwake.+ Kuwonjezera apo, anavala chilungamo monga chovala kuti akapereke chilango kwa adani ake+ ndiponso kuchita zinthu modzipereka kwambiri kunali ngati chovala chake chodula manja.+

  • Ezekieli 5:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndiyeno mkwiyo wanga udzatha+ ndipo ukali wanga ndidzauthetsera pa iwo.+ Kenako mtima wanga udzakhala pansi.+ Ndikadzathetsera ukali wanga pa iwo, pamenepo iwo adzadziwa kuti ine Yehova ndalankhula chifukwa ndimafuna kuti anthu azidzipereka kwa ine ndekha basi.+

  • Zekariya 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndiyeno mngelo amene anali kulankhula ndi ine uja anandiuza kuti: “Fuula kuti, ‘Yehova wa makamu wanena kuti: “Ndakhala ndikuchitira nsanje kwambiri Yerusalemu ndi Ziyoni.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena