Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 45:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Mulungu ndiye mpando wako wachifumu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+

      Ndodo yako yachifumu ndiyo ndodo yachilungamo.+

  • Yesaya 16:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “Mpando wachifumu ndithu udzakhazikika ndi kukoma mtima kosatha.+ Mfumu idzakhala pampandowo n’kumalamulira mokhulupirika muhema wa Davide.+ Izidzaweruza n’kumafunafuna chilungamo, ndipo izidzachita mwachangu zinthu zoyenera.”+

  • Yesaya 32:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Taonani! Mfumu+ idzalamulira mwachilungamo,+ ndipo akalonga+ adzalamuliranso mwachilungamo.

  • Yohane 5:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Ine sindingachite chilichonse chongoganiza ndekha. Ndimaweruza malinga ndi mmene ndamvera, ndipo chiweruzo chimene ndimapereka n’cholungama,+ chifukwa sinditsatira chifuniro changa, koma chifuniro+ cha amene anandituma.

  • Aheberi 1:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Koma ponena za Mwana wake, iye akuti: “Mulungu ndiye mpando wako wachifumu mpaka muyaya,+ ndipo ndodo ya ufumu+ wako ndiyo ndodo yachilungamo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena