Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 28:63
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 63 “Chotero, monga mmene Yehova anasangalalira kuti akuchitireni zabwino ndi kukuchulukitsani,+ momwemonso adzasangalala kuti akuwonongeni ndi kukufafanizani.+ Pamenepo mudzatheratu m’dziko limene mukupita kukalitenga kukhala lanu.+

  • Amosi 4:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Taona! Yehova Mulungu wa makamu ndilo dzina+ la amene anapanga mapiri,+ analenga mphepo,+ amene amafotokozera munthu zimene akuganiza,+ amene amachititsa kuwala kwa m’bandakucha kukhala mdima+ ndiponso amene amaponda malo okwezeka a dziko lapansi.”+

  • Aroma 9:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Pakuti Yehova adzazenga milandu padziko lapansi, ndi kuimaliza yonse mwachangu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena