Yeremiya 50:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Choncho anyamata ake adzaphedwa m’mabwalo a mizinda yake,+ ndipo tsiku limenelo amuna ake onse ankhondo adzaphedwa,”+ watero Yehova. Yeremiya 51:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Munthu wodziwa kukunga uta musamulole kuchita zimenezo.+ Musamulole kunyamuka kuti amenye nkhondo atavala chovala chamamba achitsulo. “Anthu inu musamvere chisoni anyamata ake.+ Wonongani gulu lake lonse la asilikali.+
30 Choncho anyamata ake adzaphedwa m’mabwalo a mizinda yake,+ ndipo tsiku limenelo amuna ake onse ankhondo adzaphedwa,”+ watero Yehova.
3 “Munthu wodziwa kukunga uta musamulole kuchita zimenezo.+ Musamulole kunyamuka kuti amenye nkhondo atavala chovala chamamba achitsulo. “Anthu inu musamvere chisoni anyamata ake.+ Wonongani gulu lake lonse la asilikali.+