Ezekieli 28:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘“Mtima wako unadzikweza chifukwa cha kukongola kwako.+ Unawononga nzeru zako chifukwa cha ulemerero wako wonyezimira.+ Ndidzakuponyera kudziko lapansi+ ndipo mafumu azidzakuyang’ana.+
17 “‘“Mtima wako unadzikweza chifukwa cha kukongola kwako.+ Unawononga nzeru zako chifukwa cha ulemerero wako wonyezimira.+ Ndidzakuponyera kudziko lapansi+ ndipo mafumu azidzakuyang’ana.+