Yobu 40:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mkwiyo wako wosefukira utuluke,+Ndipo uone aliyense wodzikweza n’kumutsitsa. Salimo 73:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndithudi, mwawaimika pamalo oterera.+Mwawagwetsa kuti awonongeke.+ Salimo 147:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova amathandiza anthu ofatsa,+Koma anthu oipa amawagwetsera pansi.+ Yesaya 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Koma adzakutsitsira ku Manda,+ pansi penipeni pa dzenje.+