Yesaya 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 M’tsiku limenelo, otsala a Isiraeli+ ndi opulumuka a nyumba ya Yakobo sadzadaliranso yemwe akuwamenya,+ koma ndi mtima wonse adzadalira Yehova, Woyera wa Isiraeli.+ Yesaya 29:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ofatsa+ adzawonjezera kukondwa mwa Yehova, ndipo ngakhale osauka pakati pa anthu adzasangalala ndi Woyera wa Isiraeli,+ Mika 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma ine ndidzadikirira Yehova.+ Ndidzayembekezera moleza mtima Mulungu wa chipulumutso changa.+ Mulungu wanga adzandimvera.+
20 M’tsiku limenelo, otsala a Isiraeli+ ndi opulumuka a nyumba ya Yakobo sadzadaliranso yemwe akuwamenya,+ koma ndi mtima wonse adzadalira Yehova, Woyera wa Isiraeli.+
19 Ofatsa+ adzawonjezera kukondwa mwa Yehova, ndipo ngakhale osauka pakati pa anthu adzasangalala ndi Woyera wa Isiraeli,+
7 Koma ine ndidzadikirira Yehova.+ Ndidzayembekezera moleza mtima Mulungu wa chipulumutso changa.+ Mulungu wanga adzandimvera.+