Yesaya 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 mwamuna wamphamvu, munthu wankhondo, woweruza, mneneri,+ wowombeza, mwamuna wachikulire,+ Yesaya 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 chotero Yehova adzadula mutu+ ndi mchira+ wa Isiraeli. Adzadulanso mphukira ndi udzu* tsiku limodzi.+ Ezekieli 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Nthawi idzakwana, tsikulo lidzafika. Wogula asasangalale+ ndipo wogulitsa asalire, pakuti mkwiyo wa Mulungu wayakira khamu lonselo. Hoseya 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Zimene zidzachitikira anthuwo zidzachitikiranso ansembe.+ Ndidzawaimba mlandu onsewa chifukwa cha njira zawo+ ndipo ndidzawabwezera zochita zawo.+
14 chotero Yehova adzadula mutu+ ndi mchira+ wa Isiraeli. Adzadulanso mphukira ndi udzu* tsiku limodzi.+
12 Nthawi idzakwana, tsikulo lidzafika. Wogula asasangalale+ ndipo wogulitsa asalire, pakuti mkwiyo wa Mulungu wayakira khamu lonselo.
9 “Zimene zidzachitikira anthuwo zidzachitikiranso ansembe.+ Ndidzawaimba mlandu onsewa chifukwa cha njira zawo+ ndipo ndidzawabwezera zochita zawo.+