-
Deuteronomo 29:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 “Ndiyeno zikachitika kuti wina amene wamva mawu a lumbiro+ ili, walankhula modzitama mumtima mwake kuti, ‘Ndidzakhala ndi mtendere+ ngakhale kuti ndidzayenda motsatira zofuna za mtima wanga,’+ koma ali ndi cholinga chowononga wina aliyense, mofanana ndi kukokolola mtengo wothiriridwa bwino ndi wosathiriridwa womwe,
-