Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 10:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Mumtima mwake amanena kuti: “Sindidzagwedezeka.+

      Palibe chimene chidzandichitikira ku mibadwomibadwo.”+

  • Yeremiya 5:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Iwo akana Yehova, ndipo akunena kuti, ‘Iye kulibe.+ Ndipo ife tsoka silidzatigwera. Sitidzaona lupanga lililonse kapena njala yaikulu.’+

  • Yeremiya 14:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Kodi Yuda mwamukaniratu,+ kapena kodi mukunyansidwa ndi Ziyoni?+ N’chifukwa chiyani mwatikantha popanda wotichiritsa?+ Anthu anali kuyembekezera mtendere, koma palibe chabwino chimene chachitika. Anali kuyembekezera nthawi yochiritsidwa, koma taonani, kukuchitika zoopsa zokhazokha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena