Yesaya 30:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Malo otchedwa Tofeti*+ owonongerako Asuri akonzedwa kale. Malowo akonzedweranso mfumu yawo.+ Malo amene iye wakonzawo ndi ozama ndipo kuli moto waukulu ndi nkhuni zambiri. Mpweya wa Yehova ukuyatsa malowo ngati mtsinje wa sulufule.+ Yeremiya 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “‘Yehova wanena kuti: “Chotero taonani! Masiku akubwera pamene sadzatchulanso malowo kuti Tofeti+ ndiponso chigwa cha mwana wa Hinomu,+ koma adzawatchula kuti chigwa chopherako anthu.
33 Malo otchedwa Tofeti*+ owonongerako Asuri akonzedwa kale. Malowo akonzedweranso mfumu yawo.+ Malo amene iye wakonzawo ndi ozama ndipo kuli moto waukulu ndi nkhuni zambiri. Mpweya wa Yehova ukuyatsa malowo ngati mtsinje wa sulufule.+
6 “‘Yehova wanena kuti: “Chotero taonani! Masiku akubwera pamene sadzatchulanso malowo kuti Tofeti+ ndiponso chigwa cha mwana wa Hinomu,+ koma adzawatchula kuti chigwa chopherako anthu.