Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 17:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Yehova anali kuchenjeza+ Aisiraeli+ ndi Ayuda+ kudzera mwa aneneri ake onse+ ndi wamasomphenya aliyense,+ kuti: “Siyani njira zanu zoipa+ ndipo sungani malamulo anga,+ mogwirizana ndi chilamulo chonse+ chimene ndinalamula makolo anu,+ ndi chimene ndinakutumizirani kudzera mwa atumiki anga, aneneri.”+

  • 2 Mbiri 30:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno asilikali othamanga+ amene anatenga makalata ochokera kwa mfumu ndi kwa akalonga ake,+ anapita mu Isiraeli ndi Yuda yense mogwirizana ndi lamulo la mfumu, lakuti: “Inu ana a Isiraeli, bwererani+ kwa Yehova Mulungu+ wa Abulahamu, Isaki ndi Isiraeli, kuti iye abwerere kwa anthu anu otsala+ amene anapulumuka m’manja mwa mafumu a Asuri.+

  • Hoseya 14:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “Iwe Isiraeli, bwerera kwa Yehova Mulungu wako+ pakuti wapunthwa mu zolakwa zako.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena