2 Mbiri 24:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yehova anapitiriza kutumiza aneneri+ pakati pawo kuti awabwezere kwa iye. Aneneriwo anapitiriza kupereka umboni wowatsutsa, koma sanamvere.+ 2 Mbiri 36:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma iwo ankangonyogodola+ amithenga a Mulungu woona, kunyoza mawu ake+ ndi kuseka+ aneneri ake, mpaka kufika poti panalibenso chiyembekezo choti angathe kuchiritsidwa.+ Kenako mkwiyo+ wa Yehova unawagwera. Aheberi 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Kalekale, Mulungu analankhula ndi makolo athu nthawi zambiri+ ndiponso m’njira zambiri kudzera mwa aneneri.+
19 Yehova anapitiriza kutumiza aneneri+ pakati pawo kuti awabwezere kwa iye. Aneneriwo anapitiriza kupereka umboni wowatsutsa, koma sanamvere.+
16 Koma iwo ankangonyogodola+ amithenga a Mulungu woona, kunyoza mawu ake+ ndi kuseka+ aneneri ake, mpaka kufika poti panalibenso chiyembekezo choti angathe kuchiritsidwa.+ Kenako mkwiyo+ wa Yehova unawagwera.
1 Kalekale, Mulungu analankhula ndi makolo athu nthawi zambiri+ ndiponso m’njira zambiri kudzera mwa aneneri.+