Levitiko 26:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ine ndidzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo ndidzakusololerani lupanga ndi kukupitikitsani.+ Dziko lanu lidzakhala bwinja,+ ndipo mizinda yanu idzawonongedwa ndi kukhala mabwinja. Yeremiya 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamene akusala kudya ine sindikumvetsera kuchonderera kwawo.+ Pamene akupereka nsembe zopsereza zathunthu ndi nsembe zambewu ine sindikukondwera nazo,+ ndipo ndiwawononga ndi lupanga, njala yaikulu ndiponso mliri.”+
33 Ine ndidzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo ndidzakusololerani lupanga ndi kukupitikitsani.+ Dziko lanu lidzakhala bwinja,+ ndipo mizinda yanu idzawonongedwa ndi kukhala mabwinja.
12 Pamene akusala kudya ine sindikumvetsera kuchonderera kwawo.+ Pamene akupereka nsembe zopsereza zathunthu ndi nsembe zambewu ine sindikukondwera nazo,+ ndipo ndiwawononga ndi lupanga, njala yaikulu ndiponso mliri.”+