1 Samueli 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho Samueli anamuuza mawu onse ndipo sanam’bisire kanthu. Pamenepo Eli anati: “Ndi Yehova amene wanena. Achite zimene akuona kuti n’zabwino.”+ 1 Mafumu 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ukamuuze kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Kodi wapha munthu+ n’kutenganso munda wake?”’+ Ukamuuzenso kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Pamalo+ amene agalu ananyambita magazi a Naboti, pomweponso agalu adzanyambita magazi ako, a iweyo.”’”+ Machitidwe 20:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pakuti sindinakubisireni kanthu, koma ndinakuuzani chifuniro+ chonse cha Mulungu.
18 Choncho Samueli anamuuza mawu onse ndipo sanam’bisire kanthu. Pamenepo Eli anati: “Ndi Yehova amene wanena. Achite zimene akuona kuti n’zabwino.”+
19 Ukamuuze kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Kodi wapha munthu+ n’kutenganso munda wake?”’+ Ukamuuzenso kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Pamalo+ amene agalu ananyambita magazi a Naboti, pomweponso agalu adzanyambita magazi ako, a iweyo.”’”+