Deuteronomo 31:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mose atangomaliza kulemba mawu onse a chilamulo ichi m’buku,+ Yeremiya 45:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Mneneri Yeremiya analankhula ndi Baruki+ mwana wa Neriya pa nthawi imene Barukiyo anali kulemba mawu a Yeremiya m’buku.+ Chimenechi chinali chaka chachinayi cha ulamuliro wa Yehoyakimu+ mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda. Yeremiyayo anati: Ezekieli 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndili mkati moyang’ana, ndinangoona dzanja litatambasukira kwa ine.+ M’dzanjalo munali mpukutu wolembedwa.+
45 Mneneri Yeremiya analankhula ndi Baruki+ mwana wa Neriya pa nthawi imene Barukiyo anali kulemba mawu a Yeremiya m’buku.+ Chimenechi chinali chaka chachinayi cha ulamuliro wa Yehoyakimu+ mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda. Yeremiyayo anati:
9 Ndili mkati moyang’ana, ndinangoona dzanja litatambasukira kwa ine.+ M’dzanjalo munali mpukutu wolembedwa.+