Yeremiya 34:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo Zedekiya mfumu ya Yuda+ ndi akalonga ake ndidzawapereka m’manja mwa adani awo, m’manja mwa anthu ofuna moyo wawo ndiponso m’manja mwa magulu ankhondo a mfumu ya ku Babulo+ amene akubwerera osakuthirani nkhondo.’+ Yeremiya 37:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno gulu lankhondo la Farao linabwera kuchokera ku Iguputo.+ Akasidi amene anali atazungulira mzinda wa Yerusalemu atamva zimenezi anachoka ku Yerusalemu.+
21 Ndipo Zedekiya mfumu ya Yuda+ ndi akalonga ake ndidzawapereka m’manja mwa adani awo, m’manja mwa anthu ofuna moyo wawo ndiponso m’manja mwa magulu ankhondo a mfumu ya ku Babulo+ amene akubwerera osakuthirani nkhondo.’+
5 Ndiyeno gulu lankhondo la Farao linabwera kuchokera ku Iguputo.+ Akasidi amene anali atazungulira mzinda wa Yerusalemu atamva zimenezi anachoka ku Yerusalemu.+