Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 25:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Akuluakulu onse a magulu ankhondo+ ndi asilikali awo atamva kuti mfumu ya Babulo yasankha Gedaliya, nthawi yomweyo anapita kwa Gedaliya ku Mizipa.+ Akuluakuluwo anali Isimaeli mwana wa Netaniya, Yohanani mwana wa Kareya, Seraya mwana wa Tanumeti Mnetofa, ndi Yaazaniya mwana wa Amaakati, pamodzi ndi asilikali awo.

  • Yeremiya 40:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Iwo anauza Gedaliya kuti: “Kodi sukudziwa kuti Baalisi mfumu ya ana a Amoni+ watumiza Isimaeli+ mwana wa Netaniya+ kuti adzakuphe?” Koma Gedaliya mwana wa Ahikamu sanakhulupirire zimenezo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena