Ezara 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako ndinalamula kuti tisale kudya tili kumtsinje wa Ahava kuja, kuti tidzichepetse+ pamaso pa Mulungu wathu ndi kumupempha kuti atisonyeze njira yoyenera+ kwa ife, ana athu,+ ndi katundu wathu yense. Miyambo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Uzim’kumbukira m’njira zako zonse,+ ndipo iye adzawongola njira zako.+
21 Kenako ndinalamula kuti tisale kudya tili kumtsinje wa Ahava kuja, kuti tidzichepetse+ pamaso pa Mulungu wathu ndi kumupempha kuti atisonyeze njira yoyenera+ kwa ife, ana athu,+ ndi katundu wathu yense.