Yeremiya 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yerusalemu ndidzamusandutsa milu ya miyala+ ndiponso malo obisalamo mimbulu.+ Mizinda ya Yuda ndidzaisandutsa mabwinja, malo opanda wokhalamo.+ Maliro 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Amene anali ndi anthu ambiri+ tsopano wakhala wopanda anthu.+Amene anali ndi anthu ambiri pakati pa mitundu ina+ wakhala ngati mkazi wamasiye.+Amene anali wolemekezeka pakati pa zigawo zina wayamba kugwira ntchito yaukapolo.+
11 Yerusalemu ndidzamusandutsa milu ya miyala+ ndiponso malo obisalamo mimbulu.+ Mizinda ya Yuda ndidzaisandutsa mabwinja, malo opanda wokhalamo.+
1 Amene anali ndi anthu ambiri+ tsopano wakhala wopanda anthu.+Amene anali ndi anthu ambiri pakati pa mitundu ina+ wakhala ngati mkazi wamasiye.+Amene anali wolemekezeka pakati pa zigawo zina wayamba kugwira ntchito yaukapolo.+