Ezara 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano pambuyo pa zonse zimene zatigwera chifukwa cha zochita zathu zoipa+ ndi machimo athu ochuluka, ngakhale kuti inuyo Mulungu wathu simunatilange monga mmene tinafunika kulangidwira+ ndipo mwalola kuti anthu onsewa apulumuke,+ Nehemiya 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene anasungunula chitsulo n’kudzipangira chifanizo cha mwana wa ng’ombe+ n’kuyamba kunena kuti, ‘Uyu ndiye Mulungu wanu, Aisiraeli inu, amene anakutulutsani mu Iguputo,’+ ndipo anachita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani, Danieli 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Sitinamvere atumiki anu aneneri,+ amene analankhula m’dzina lanu kwa mafumu athu, akalonga athu, makolo athu, ndi anthu onse a m’dziko lathu.+
13 Tsopano pambuyo pa zonse zimene zatigwera chifukwa cha zochita zathu zoipa+ ndi machimo athu ochuluka, ngakhale kuti inuyo Mulungu wathu simunatilange monga mmene tinafunika kulangidwira+ ndipo mwalola kuti anthu onsewa apulumuke,+
18 Pamene anasungunula chitsulo n’kudzipangira chifanizo cha mwana wa ng’ombe+ n’kuyamba kunena kuti, ‘Uyu ndiye Mulungu wanu, Aisiraeli inu, amene anakutulutsani mu Iguputo,’+ ndipo anachita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani,
6 Sitinamvere atumiki anu aneneri,+ amene analankhula m’dzina lanu kwa mafumu athu, akalonga athu, makolo athu, ndi anthu onse a m’dziko lathu.+