Numeri 21:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Choncho Aisiraeli analanda mizinda yonseyi n’kuyamba kukhala m’mizinda yonse ya Aamori+ ku Hesiboni,+ ndi m’midzi yake yonse yozungulira. Yoswa 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mizinda yotsatirayi ya m’gawo la Isakara ndi Aseri, pamodzi ndi anthu ake ndi midzi yake yozungulira, inali ya Manase:+ Beti-seani,+ Ibuleamu,+ Dori,+ Eni-dori,+ Taanaki,+ ndi Megido.+ Madera atatu amapiri analinso ake.
25 Choncho Aisiraeli analanda mizinda yonseyi n’kuyamba kukhala m’mizinda yonse ya Aamori+ ku Hesiboni,+ ndi m’midzi yake yonse yozungulira.
11 Mizinda yotsatirayi ya m’gawo la Isakara ndi Aseri, pamodzi ndi anthu ake ndi midzi yake yozungulira, inali ya Manase:+ Beti-seani,+ Ibuleamu,+ Dori,+ Eni-dori,+ Taanaki,+ ndi Megido.+ Madera atatu amapiri analinso ake.