Yesaya 32:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu akazi amene mukukhala mosatekeseka, njenjemerani! Inu osasamala, chitani mantha! Vulani n’kukhala maliseche, ndipo muvale ziguduli m’chiuno mwanu.+ Yeremiya 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pachifukwa chimenechi valani ziguduli,* anthu inu.+ Dzigugudeni pachifuwa ndi kulira mofuula,+ chifukwa mkwiyo woyaka moto wa Yehova sunatichokere.+ Yeremiya 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Iwe mwana wamkazi wa anthu anga, vala chiguduli*+ ndi kuvimvinizika m’phulusa.+ Lira ngati kuti ukulira maliro a mwana wamwamuna mmodzi yekhayo. Lira mowawidwa mtima+ chifukwa wofunkha adzatiukira modzidzimutsa.+
11 Inu akazi amene mukukhala mosatekeseka, njenjemerani! Inu osasamala, chitani mantha! Vulani n’kukhala maliseche, ndipo muvale ziguduli m’chiuno mwanu.+
8 Pachifukwa chimenechi valani ziguduli,* anthu inu.+ Dzigugudeni pachifuwa ndi kulira mofuula,+ chifukwa mkwiyo woyaka moto wa Yehova sunatichokere.+
26 Iwe mwana wamkazi wa anthu anga, vala chiguduli*+ ndi kuvimvinizika m’phulusa.+ Lira ngati kuti ukulira maliro a mwana wamwamuna mmodzi yekhayo. Lira mowawidwa mtima+ chifukwa wofunkha adzatiukira modzidzimutsa.+