Yeremiya 48:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu mudzagwidwa ndi adani chifukwa mukudalira ntchito zanu ndi chuma chanu.+ Kemosi+ adzatengedwa kupita ku ukapolo+ pamodzi ndi ansembe ake ndi akalonga ake.+ Amosi 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo mfumu yawo idzagwidwa ndi kupita ku ukapolo pamodzi ndi akalonga ake,”+ watero Yehova.’
7 Inu mudzagwidwa ndi adani chifukwa mukudalira ntchito zanu ndi chuma chanu.+ Kemosi+ adzatengedwa kupita ku ukapolo+ pamodzi ndi ansembe ake ndi akalonga ake.+