Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 50:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Iwe umadana ndi malangizo,*+

      Ndipo umaponya mawu anga kunkhongo.+

  • Yesaya 1:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Kodi mumenyedwanso pati+ mmene mukupitiriza kupandukamu?+ Mutu wanu uli ndi zilonda zokhazokha, ndipo mtima wanu wafooka.+

  • Yesaya 42:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Choncho Mulungu anali kuwakhuthulira mkwiyo, ukali wake, ndi nkhondo yoopsa.+ Nkhondoyo inali kuwapsereza+ koma iwo sanazindikire.+ Inapitiriza kuwatentha koma iwo sanaganizire chilichonse mumtima mwawo.+

  • Yeremiya 7:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Ukawauze kuti, ‘Uwu ndiwo mtundu umene anthu ake sanamvere mawu a Yehova Mulungu wawo,+ ndipo sanamvere chilango.*+ Palibe munthu wokhulupirika pakati pawo, ndipo satchulanso n’komwe za kukhulupirika.’+

  • Zefaniya 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Mzindawo sunafune kumvera,+ sunalole kulangizidwa,*+ sunakhulupirire Yehova+ ndipo sunayandikire Mulungu wake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena