Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 33:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Yehova anapitiriza kulankhula kwa Manase ndi anthu ake, koma iwo sanamvere.+

  • Yeremiya 11:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Koma iwo sanamvere kapena kutchera khutu.+ M’malomwake aliyense wa iwo anapitiriza kuumitsa mtima wake woipawo.+ Choncho ndinawalanga mogwirizana ndi mawu onse amene ndinanena m’pangano langa, amene ndinawalamula kuti awasunge, koma sanawasunge.’”

  • Yeremiya 17:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Koma iwo sanamvere kapena kutchera khutu+ moti anapitiriza kuumitsa khosi+ lawo kuti asamve ndi kulandira mwambo.”’*+

  • Yeremiya 25:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Kuyambira m’chaka cha 13 cha ulamuliro wa Yosiya+ mwana wa Amoni, mfumu ya Yuda, kufikira lero, zaka 23 zonsezi, Yehova wakhala akundiuza mawu ndipo ine ndakhala ndikukuuzani mawuwo, kudzuka m’mawa kwambiri ndi kukuuzani mawu akewo koma simunandimvere.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena