Salimo 146:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova adzakhala mfumu mpaka kalekale,+Mulungu wako, iwe Ziyoni, adzakhala mfumu ku mibadwomibadwo.+Tamandani Ya, anthu inu!+ Salimo 149:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Isiraeli asangalale ndi Womupanga Wamkulu,+Ana a Ziyoni akondwere ndi Mfumu yawo.+ Yesaya 33:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti Yehova ndiye Woweruza wathu.+ Yehova ndiye Wotipatsa Malamulo.+ Yehova ndiye Mfumu yathu.+ Iye adzatipulumutsa.+
10 Yehova adzakhala mfumu mpaka kalekale,+Mulungu wako, iwe Ziyoni, adzakhala mfumu ku mibadwomibadwo.+Tamandani Ya, anthu inu!+
22 Pakuti Yehova ndiye Woweruza wathu.+ Yehova ndiye Wotipatsa Malamulo.+ Yehova ndiye Mfumu yathu.+ Iye adzatipulumutsa.+