Ekisodo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndi mulungu wina uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+Ndinu woyera kopambana, ndani angafanane ndi inu?+Ndinu woyenera kuopedwa+ ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda.+ Inu ndinu wochita zodabwitsa.+ 2 Samueli 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 N’chifukwa chake ndinudi wokwezeka,+ inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa. Ngakhale kuti tamva za milungu ina yambirimbiri, palibe Mulungu wina+ koma inu nokha.+ Salimo 86:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova, palibe mulungu wina amene angafanane ndi inu.+Ndipo palibe ntchito zilizonse zofanana ndi ntchito zanu.+
11 Ndi mulungu wina uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+Ndinu woyera kopambana, ndani angafanane ndi inu?+Ndinu woyenera kuopedwa+ ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda.+ Inu ndinu wochita zodabwitsa.+
22 N’chifukwa chake ndinudi wokwezeka,+ inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa. Ngakhale kuti tamva za milungu ina yambirimbiri, palibe Mulungu wina+ koma inu nokha.+
8 Inu Yehova, palibe mulungu wina amene angafanane ndi inu.+Ndipo palibe ntchito zilizonse zofanana ndi ntchito zanu.+